Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 5:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ciri conse cabadwa mwa Mulungu cililaka dziko lapansi; ndipo ici ndi cilako tililaka naco dziko lapansi, ndico cikhulupiriro cathu.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 5

Onani 1 Yohane 5:4 nkhani