Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 5:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tidziwa kuti Mwana wa Mulungu wafika, natipatsa ife cidziwitso, kuti tizindikire Woonayo, ndipo tiri mwa Woonayo, mwa Mwana wace Yesu Kristu. Iye ndiye Mulungu woona ndi moyo wosatha.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 5

Onani 1 Yohane 5:20 nkhani