Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 4:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ife tazindikira, ndipo takhulupirira cikondico Mulungu ali naco pa ife. Mulungu ndiye cikondi, ndipo iye amene akhala m'cikondi akhala mwa Mulungu, ndipo Mulungu akhala mwa iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 4

Onani 1 Yohane 4:16 nkhani