Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 3:23-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Ndipo 4 Lamulo lace ndi ili, kuti tikhulupirire dzina la Mwana wace Yesu Kristu, ndi 5 kukondana wina ndi mnzace, monga anatilamulira.

24. Ndipo 6 munthu amene asunga malamulo ace akhala mwa iye, ndi iye mwa munthuyo. Ndipo 7 m'menemo tizindikira kuti akhala mwa ife, kucokera mwa Mzimu amene anatipatsa ife.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 3