Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iye amene ali naco coma ca dziko lapansi, naona mbale wace ali wosowa ndi kutsekereza cifundo cace pommana iye, nanga cikondi ca Mulungu cikhala mwa iye bwanji?

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 3

Onani 1 Yohane 3:17 nkhani