Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, cikondico Atate watipatsa, kuti tichedwe ana a Mulungu; ndipo tiri ife otere. Mwa ici dziko lapansi silizindikira ife, popeza silimzindikira iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 3

Onani 1 Yohane 3:1 nkhani