Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndakulemberani, atate, popeza mwamzindikira iye amene ali kuyambira paciyambi. Ndakulemberani, anyamata, popeza muti amphamvu, ndi mau a Mulungu akhala mwa inu, ndipo mwamlaka woipayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 2

Onani 1 Yohane 2:14 nkhani