Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 2:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tiana tanga, izi ndikulemberani, kuti musacimwe. Ndipo akacimwa wina, Nkhoswe tiri naye kwa Atate, ndiye Yesu Kristu wolungama;

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 2

Onani 1 Yohane 2:1 nkhani