Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Timoteo 6:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Limba nayo nkhondo yabwino ya cikhulupiriro, gwira moyo wosatha, umene adakuitanira, ndipo wabvomereza cibvomerezo cabwino pamaso pa mboni zambiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 6

Onani 1 Timoteo 6:12 nkhani