Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Timoteo 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti iwo akutumikira bwino adzitengera okha mbiri yabwino, ndi kulimbika kwakukuru m'cikhulupiriro ca mwa Kristu Yesu.

Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 3

Onani 1 Timoteo 3:13 nkhani