Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Petro 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akulu tsono mwa inu ndiwadandaulira, ine mkulu mnzanu ndi mboni ya zowawa za Kristu, ndinenso wolawana nao ulemerero udzabvumbulutsikawo:

Werengani mutu wathunthu 1 Petro 5

Onani 1 Petro 5:1 nkhani