Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Petro 4:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akalankhula wina, alankhule ngati manenedwe a Mulungu; wina akatumikira, acite ngati mu mphamvu imene Mulungu ampatsa, kuti m'zonse Mulungu alemekezedwe mwa Yesu Kristu, amene ali nao ulemerero ndi mphamvu ku nthawi za nthawi. Amen.

Werengani mutu wathunthu 1 Petro 4

Onani 1 Petro 4:11 nkhani