Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Petro 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemonso amuna inu, khalani nao monga mwa cidziwitso, ndi kucitira mkazi ulemu, monga cotengera cocepa mphamvu, monganso wolowa nyumba pamodzi wa cisomo ca moyo, kuti mapemphero anu angaletsedwe.

Werengani mutu wathunthu 1 Petro 3

Onani 1 Petro 3:7 nkhani