Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Petro 2:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kwa inu tsono akukhulupira, ali wa mtengo wace; koma kwa iwo osakhulupira,Mwala umene omangawo anaukana,Womwewo unayesedwa mutu wa pangondya;

Werengani mutu wathunthu 1 Petro 2

Onani 1 Petro 2:7 nkhani