Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Petro 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wodalitsika Mulungu ndiye Atate wa Ambuye wathu Yesu Kristu, iye amene, monga mwa cifundo cace cacikuru, anatibalanso ku ciyembekezo ca moyo, mwa kuuka kwa akufa kwa Yesu Kristu;

Werengani mutu wathunthu 1 Petro 1

Onani 1 Petro 1:3 nkhani