Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Petro 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kwa iwo amene kudabvumbulutsidwa, kuti sanadzitumikira iwo okha, koma inu, ndi zinthu izi, zimene zauzidwa kwa inu tsopano, mwa iwo amene anakulalikirani Uthenga Wabwino mwa Mzimu Woyera, wotumidwa kucokera Kumwamba; zinthu izi angelo alakalaka kusuzumiramo.

Werengani mutu wathunthu 1 Petro 1

Onani 1 Petro 1:12 nkhani