Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Atesalonika 4:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cotsalira tsono, abale, tikupemphani ndi kukudandaulirani mwa Ambuye Yesu, kuti, monga munalandira kwa ife mayendedwe okoma, muyenera kuyendanso ndi kukondweretsa Mulungu, monganso mumayenda, eurukani koposa momwemo.

2. Pakuti mudziwa malangizo amene tinakupatsani mwa Ambuye Yesu.

Werengani mutu wathunthu 1 Atesalonika 4