Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ine sindinacita nako kanthu kaizi; ndipo sindilemba izi kuti cikakhale cotero ndi ine; pakuti kundikomera ine kufa, koma wina asayese kwacabe kudzitamanda kwanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 9

Onani 1 Akorinto 9:15 nkhani