Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 8:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu cidziwitso siciri mwa onse; koma ena, ozolowera fano kufikira tsopano, adyako monga yoperekedwa nsembe kwa fano; ndipo cikumbu mtima cao, popeza ncofoka, cidetsedwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 8

Onani 1 Akorinto 8:7 nkhani