Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 8:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma za zoperekedwa nsembe kwa mafano: Tidziwa kuti tid naco cidziwitso tonse. Cidziwitso citukumula, koma cikondicimangirira.

2. Ngati wina ayesa kuti adziwa kanthu sanayambe kudziwa monga ayenera kudziwa.

3. Koma ngati wina akonda Mulungu, yemweyu adziwika ndi iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 8