Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 7:39-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

39. Mkazi amangika pokhala mwamuna wace ali ndi moyo; koma atamwalira mwamuna ali womasuka, kuti akwatiwe naye amene afuna, koma mwa Ambuye.

40. Koma akhala wokondwera koposa ngati akhala monga momwe ali, monga mwa kuyesa kwanga; ndipo ndiganiza kuti inenso ndiri naye Mzimu wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7