Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 7:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma wina akayesa kuti acitira mwana wace wamkazi cosamuyeoera, ngati palikupitirira pa unamwali wace, ndipo kukafunika kutero, acite cimene afuna, sacimwa; akwatitsidwe.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7

Onani 1 Akorinto 7:36 nkhani