Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 7:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mkazi wokwatiwa ndi namwali asiyananso iye wosakwatiwa alabadira za. Ambuye, kuti akhale woyera m'thupi ndi mumzimu; koma wokwatiwayo, alabadira za dziko lapansi, kuti akondweretse mwamunayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7

Onani 1 Akorinto 7:34 nkhani