Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 6:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Kodiakhoza winawa inu, pamene ali nao mlandu pa mnzace, kupita kukaweruzidwa kwa osalungama, osati kwa oyera mtima?

2. Kapena kodi simudziwa kuti oyera mtima adzaweruza dziko lapansi? Ndipo ngati dziko lapansi liweruzidwa ndi inu, muli osayenera kodi kuweruza timilandu tocepacepa?

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 6