Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 2:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo ine, abale, m'mene ndinadza kwa inu, sindinadza ndi kuposa kwa mau, kapena kwa nzeru, polalikira kwa inu cinsinsi ca Mulungu.

2. Pakuti ndinatsimikiza mtima kuti ndisadziwe kanthu mwa inu koma Yesu Kristu, ndi iye wopacikidwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 2