Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 16:22-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Ngati wina sakonda Ambuye, akhale wotembereredwa. Akudza Ambuye.

23. Cisomo ca Ambuye Yesu Kristu cikhale ndi inu.

24. Cikondi canga cikhale ndi inu nonse mwa Kristu Yesu. Amen.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 16