Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 15:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati si kutero, adzacita ciani iwo amene abatizidwa cifukwa ca akufa? Ngatiakufa saukitsidwa konse, abatizidwa cifukwa ninji cifukwa ca iwo?

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 15

Onani 1 Akorinto 15:29 nkhani