Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 14:39-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

39. Cifukwa cace; abale anga, funitsitsani kunenera, ndipo musaletse kulankhula malilime.

40. Koma zonse zicitike koyenera ndi kolongosoka.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 14