Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 14:34-36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

34. Akazi akhale cete m'Mipingo. Pakuti vsikuloledwa kwa iwo kulankhula, Koma akhale omvera, mongansocilamulo cmena,

35. Koma ngati afuna kuphunzirakanthu afunseamuna ao aiwo okha kwao; pakuti kunyazitsa mkazi kulankhula mu Mpingo.

36. Kodi mau a Mulungu anatutuka kwa iw? kapena anafika kwa inu nokha?

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 14