Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 14:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanga ciani tsono, abale? Pamene musonkhana, yense ali nalo salmo, ali naco ciphunzitso, ali nalo bvumbulutso, ali nalo lilime, ali naco cimasuliro. Mucite zonse kukumangirira.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 14

Onani 1 Akorinto 14:26 nkhani