Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 12:29-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

29. Kodi ali onse atumwi? Ali aneneri onse kodi? Ali aphunzitsi onse? Ali onse ocita zozizwa?

30. Ali nazo mphatso za maciritso onse kodi? Kodi onse alankhula ndi malilime? Kodi onse amasulira mau?

31. Koma funitsitsani mphatso zoposa. Ndipo ndikuonetsani njira yokoma yoposatu.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 12