Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 12:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakutinso mwa Mzimu mmodzi ife tonse rinabatizidwa kulowa m'thupi limodzi, ngakhale Ayuda, ngakhale Ahelene, ngakhale akapolo, ngakhale mfulu; ndipo tonse tinamwetsedwa Mzimu mmodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 12

Onani 1 Akorinto 12:13 nkhani