Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 11:31-34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. Koma ngati tikadadzizindikira tokha sitikadaweruzidwa.

32. Koma poweruzidwa, tilangidwa ndi Ambuye, kuti tingatsutsidwe pamodzi ndi dziko lapansi.

33. Cifukwa cace, abale anga, posonkhanira kudya, lindanani.

34. Ngati wina ali ndi njala adye-kwao; kuti mungasonkhanire kwa ciweruziro. Koma zotsalazo nelidzafotokoza pakudza ine.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 11