Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 11:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndifunakuti mudziwe, kuti mutu wa munthu yense ndiye Kristu; ndi mutu wa mkazi ndiye mwamuna; ndipo mutu wa Kristu ndiye Mulungu,

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 11

Onani 1 Akorinto 11:3 nkhani