Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 10:24-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Munthu asafune zace za iye yekha, kama za mnzace.

25. Conse cogulitsidwa pa msika wa nyama, mudye, osafunsa kanthu cifukwa ca cikumbu mtima;

26. pakuti dziko lapansi liri la Ambuye, ndi kudzala kwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 10