Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 10:22-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Kapena kodi ticititsa nsanje Ambuye? Kodi mphamvu zathu ziposa iye?

23. Zinthu zonse ziloleka; koma sizipindula zonse. Zinthu zonse ziloleka; koma sizimanga zonse.

24. Munthu asafune zace za iye yekha, kama za mnzace.

25. Conse cogulitsidwa pa msika wa nyama, mudye, osafunsa kanthu cifukwa ca cikumbu mtima;

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 10