Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 1:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Cisomo kwa inu ndi mtendere zocokera kwa Mulungu Atate wathu, ndi Ambuye Yesu Kristu.

4. Ndiyamika Mulungu wanga nthawi yonse kaamba ka inu, cifukwa ca cisomo ca Mulungu cinapatsidwa kwa inu mwa Kristu Yesu;

5. kuti m'zonse muoalemezedwa mwa iye, m'mau onse, ndi cidziwitso conse;

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 1