Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 1:29-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

29. 6 kuti thupi liri lonse lisadzitamande pamaso pa Mulungu.

30. Koma kwa iye muli inu mwa Kristu Yesu, 7 amene anayesedwa kwa ife nzeru ya kwa Mulungu, ndi cilungamo ndi ciyeretso ndi ciombolo;

31. kuti monga mwalembedwa, iye amene adzitamanda, adzitamande mwa Ambuye.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 1