Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 1:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa kuti copusa ca Mulungu ciposa anthu ndi nzeru zao; ndipo cofoka ca Mulunguciposa anthu ndi mphamvu yao.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 1

Onani 1 Akorinto 1:25 nkhani