Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 6:2-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Ku gareta woyamba kunali akavalo ofiira; ndi ku gareta waciwiri akavalo akuda;

3. ndi ku gareta wacitatu akavalo oyera; ndi ku gareta wacinai akavalo olimba amawanga.

4. Ndipo ndinayankha ndinati kwa mthenga wolankhula ndi ine, Izi nziani, mbuyanga?

Werengani mutu wathunthu Zekariya 6