Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 4:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anayankha, nanena kwa ine, ndi kuti, Awa ndi mau a Yehova kwa Zerubabele, Ndi khamu la nkhondo ai, ndi mphamvu ai, koma ndi Mzimu wanga, ati Yehova wa makamu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 4

Onani Zekariya 4:6 nkhani