Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti wapeputsa tsiku la tinthu tating'ono ndani? pakuti adzakondwera, asanu ndi awiri awa, nadzaona cingwe colungamitsira ciriri m'dzanja la Zerubabele, ndiwo maso a Yehova; ayendayenda mwa dziko lonse.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 4

Onani Zekariya 4:10 nkhani