Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu: Ukadzayenda m'njira zanga, ndi kusunga udikiro wanga, pamenepo udzaweruza nyumba yanga, ndi kusunga mabwalo anga, ndipo ndidzakupatsa malo oyendamo mwa awa oimirirapo.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 3

Onani Zekariya 3:7 nkhani