Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 3:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Satana, Yehova akudzudzula, Satana iwe; inde Yehova amene anasankha Yerusalemu akudzudzula; uyu sindiye muuni wofumulidwa kumoto?

Werengani mutu wathunthu Zekariya 3

Onani Zekariya 3:2 nkhani