Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 14:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inde mbiya zonse za m'Yerusalemu ndi m'Yuda zidzakhala zopatulikira Yehova wa makamu; ndi onse akuphera nsembe adzafika nadzatengako, ndi kuphikamo; ndipo tsiku lomwelo simudzakhalanso Mkanani m'nyumba ya Yehova wa makamu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 14

Onani Zekariya 14:21 nkhani