Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 14:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dziko lonse lidzasandulika, lidzanga cidikha, kuyambira ku Geba kufikira ku Rimoni, kumwela kwa Yerusalemu; ndipo pali uwupo padzakhala ponyamuka, ndipo udzakhala m'malo mwace, kuyambira ku cipata ca Benjamini kufikira ku malo a cipata coyamba, kufikira ku cipata ca kungondya, ndi kuyambira nsanja ya Hananeli kufikira ku zoponderamo mphesa za mfumu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 14

Onani Zekariya 14:10 nkhani