Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pfuulanso, ndi kuti, Atero Yehova wa makamu: Midzi yanga idzalemerera ndi kufalikiranso; ndipo Yehova adzasangalatsanso Ziyoni, nadzasankhamo Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 1

Onani Zekariya 1:17 nkhani