Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zefaniya 3:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti pamenepo ndidzapatsa mitundu ya anthu mlomo woyera, kuti onsewa aitanire pa dzina la Yehova kumtumikira ndi mtima umodzi.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3

Onani Zefaniya 3:9 nkhani