Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zefaniya 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Otsala a Israyeli sadzacita cosalungama, kapena kunena mabodza; ndi m'kamwa mwao simudzapezeka lilime lonyenga; pakuti adzadya nadzagona pansi, ndi palibe wakuwaopsa.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3

Onani Zefaniya 3:13 nkhani