Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zefaniya 3:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Tsoka uyo wopanduka, ndi wodetsedwa, ndiye mudzi wozunza!

2. Sanamvera mau, sanalola kulangizidwa; sanakhulupirira Yehova, sanayandikira kwa Mulungu wace.

3. Akalonga ace m'kati mwace ndiwo mikango yobangula; oweruza ace ndi mimbulu ya madzulo, sasiya kanthu ka mawa.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3